Skip to main content

Full text of "Chikalakala Chakuyamba Cha Musa, Chimatanidwa"

See other formats


CHIKALAKALA CHAKUYAMBA CHA MUSA, 
CHIMATANIDWA 



GENESIS 



1PAKUYAMBA Mlungu adapanga 
Kumwamba ndi j iko. 2 Ndi j iko lidali 
lotimbilikanya ndi lopanda malile ; ndi 
mdima udalipo pamwamba pa nkope ya 
vindimba: ndi roho ya Mlungu chiuta- 
mile pamwamba pa nkope ya maji. 
3 Naati Mlungu, Likalepo dangalila : 
ndipo lidakalapo dangalila. 4 Naaliona 
Mlungu dangalila, kuti labwino : naapa- 
tula Mlungu dangalila ndi mdima. 5 Na- 
alitana Mlungu dangalila Usana, ndi 
mdima adautana TJsiku. Ndipo udalipo 
ujulo ndipo udalipo umawa, siku limoji. 

6 Naati Mlungu, Ukalepo mlengalenga 
pakati pa maji, chipatulile maji ndi 
maji. 7 Naauchita Mlungu mlengalenga, 
naapatula maji yayo yadali panchi pa 
mlengalenga- ndi maji yayo yadali pa- 
mwamba pa mlengalenga : ndipo idalipo 
chimwechi. 8 Naautana Mlungu mle- 
ngalenga Kumwamba. Ndipo udalipo 
ujulo ndipo udalipo umawa, siku la 
kawili. 

9 Naati Mlungu, Maji yayo yali panchi 
pa Kumwamba yakusidwe pa malo pa- 
moji, ndi uoneke mtunda : ndipo idalipo 
chimwechi. 10 Naautana Mlungu mtu- 
nda Jiko; ndi paja maji yadakusidwa 
adapatana Zinyanja : naaona Mlungu 
kuti ehabwino. 11 Naati Mlungu, Lime- 
leche jiko mopo, mmela wakumwazika 
mbeu,mtengo wa vipacho wopacha vipacho 
kwamtundu wake, uwo mbeu yake mkati 
mwake, pamwamba pa jiko : ndipo idalipo 
chimwechi. 12 Ndipo jiko lidatulueha 
mopo, mmela wakumwazika mbeu kwa 
mtundu wake, ndi mtengo wakupacha 
vipacho, uwo mbeu yake mkati mwake, 
kwa mtundu wake : naaona Mlungu kuti 
ehabwino. 13 Ndipo udalipo ujulo ndipo 
udalipo umawa, siku la katatu. 



14 Naati Mlungu, Ikalepo mienje pa 
mlengalenga wa Kumwamba kupatula 
usana ndi usiku ; ndipo ikale kwa vizi- 
ndikilo, ndi kwa zinyengo, ndi kwa ma- 
siku ndi vyaka : 15 ndi ikale kwa mienje 
pa mlengalenga wa Kumwamba kumulika 
pamwamba pa jiko : ndipo idalipo chi- 
mwechi. 16 Naaichita Mlungu mienje 
yaikulu iwili ; mwenje wokulu kuulinga- 
nicha usana, ndi mwenje wong'ono ndi 
ntondwa kuulinganicha usiku. 17 Naa- 
ziika Mlungu izo pa mlengalenga wa 
Kumwamba kumulika pamwamba pa jiko, 
18 ndi kuulinganicha usana ndi usiku, 
ndi kupatula dangalila ndi mdima : naao- 
na Mlungu kuti ehabwino. 19 Ndipo 
udalipo ujulo ndipo udalipo umawa, siku 
la kanai. 

20 Naati Mlungu, Maji yatutumiche 
chotutuma chene umoyo chakulama, ndi 
chakuuluka chiuluke pamwamba pa jiko 
pamwamba pa nkope ya mlengalenga wa 
Kumwamba. 21 Naayapanga Mlungu 
mafuni yakulu, ndi chene umoyo chili 
chonche chakulama chakuseta, ivo maji 
yadavitutumicha, kwa mitundu yao, ndi 
chakuuluka chene mapapiko chili chonche 
kwa mtundu wake : naaona Mlungu kuti 
ehabwino. 22 Naayapacha Mlungu achi- 
iwo mwawi, kuti, Mbalane, mchuruke, 
ndipo myazaze maji pa nyanja, ndi 
chakuuluka ehiehuruke pa jiko. 23 Ndi- 
no udalipo ujulo ndipo udalipo umawa, 
siku la kasano ndi kamoji. 

24 Naati Mlungu, Jiko lituluche chene 
umoyo chakulama kwa mtundu wake, 
chilangwa, ndi chakuseta, ndi chikoko 
cha pa jiko kwa mtundu wake : ndipo ida- 
lipo chimwechi. 25 Naachichita Mlungu 
chikoko cha pa jiko kwa mtundu wake, 
ndi chilangwa kwa mtundu wake, ndi 



1. 26—2. 22 



GENESIS 



chakuseta chili chonche pa ntaka kwa 
mtundu wake: naaona Mlungu kuti 
chabwino. 26 Naati Mlungu, Timchite 
muntu pa chitunjitunji cha ife, kufwana- 
na ndi ife : ndi waigwirize nchomba 
ya pa nyanja mwendo, ndi chakuuluka 
cha Kumwamba, ndi chilangwa, ndi jiko 
lonche, ndi chakuseta chili chonche chi- 
setacho pamwamba pa jiko. 27 Naampa- 
nga Mlungu muntu pa chitunjitunji cha 
iye, pa chitunjitunji cha Mlungu ada- 
mpanga iye; wamwamuna ndi wamkazi 
adawapanga achiiwo. 28 Naawapacha 
Mlungu achiiwo mwawi«: naati Mlungu 
kwa achiiwo, Mbalane, mchumke, ndipo 
mlizaze jiko, mlipondele ; ndipo mgwi- 
rize nchomba ya pa nyanja mwendo, 
ndi chakuuluka cha Kumwamba, ndi 
chintu chili chonche chakulama icho 
chisetacho pamwamba pa jiko. 29 Naati 
Mlungu, Penya, ndakupachani mmela uli 
wonche wakumwazika mbeu, uwo panwa- 
mba pa nkope ya jiko lonche, ndi mtengo 
uli wonche, uwo uli ndi vipacho va 
mtengo mkati mwake wakumwazika 
mbeu ; kwa inu siukale kwa chakudya : 
30 ndi kwa chikoko chili chonche cha pa 
jiko, ndi kwa chakuuluka chili chonche 
cha Kumwamba, ndi kwa chintu chili 
chonche chakuseta pamwamba pa jiko, 
icho chili ndi chene umoyo chakulama 
mkati mwake, ndapeleka mmela uli 
wonche wowisi kwa chakudya : ndipo ida- 
lipo chimwechi. 31 Naachiona Mlungu 
chintu chili chonche icho anachichita, 
ndipo, penya, chabwino viwi. Ndipo 
udalipo ujulo ndipo udalipo umawa, siku 
la kasano ndi kamoji. 

2 Ndi kudamalizika Kumwamba ndi 
jiko, ndi liwanja la.o lonche. 2 Na- 
amaliza siku la kasano ndi kawili Mlungu 
chotumika chake icho anachichita ; na- 
apuma siku la kasano ndi kawili pa 
chotumika chake chonche icho anachi- 
chita. 3 Naapacha Mlungu siku la 
kasano ndi kawili mwawi, naaliika li- 
mwelo paloka : chifuko pa limwelo ana- 
puma pa chotumika chake chonche icho 
anachipanga Mlungu kuchichita. 

4 Ivi vibadwa va Kumwamba ndi va 
jiko pa kupangidwa kwao, pa siku ilo 
Yahveh Mlungu adachita jiko ndi Ku- 
mwamba. 5 Ndi chakupuka chili chonche 
cha pa dambo sichinakalepo pa jiko, ndi 
mmela uli wonche wa pa dambo sunapu- 
ke : chifuko Yahveh Mlungu sanavu- 



6 



mbicha vula pa jiko, ndi padalije muntu 
kulima pa ntaka ; 6 nampo chidakwela 
chipundulu pa jiko, ndi kuimwecha nkope 
yonche ya ntaka. 7 Naamumba Yahveh 
Mlungu muntu ndi lifumbi la ntaka, naa- 
pumilila pa mpuno zake mpuye wa kula- 
ma ; naapata muntu kukala mwene umoyo 
wakulama. 8 Naavyala Yahveh Mlungu 
munda pa Eden, kuvuma; naamwika 
pamwepo muntu uyo adamumba. 9 Na- 
apukicha Yahveh Mlungu pa ntaka mte- 
ngo uli wonche wakumbika kwa kuonekela, 
ndi wabwino kwa chakudya ; mtengo wa 
kulama ncho pakati pa munda, ndi mte- 
ngo wa kujiwa vabwino ndi voipa. 
10 Ndi mchinje udaturuka pa Eden 
kuumwecha munda maji ; ndi kuchoka 
pamwepo udajipatula, kupata kukala mitu 
inai. 11 Jina la wakuyamba Pishon : 
umwewo wakulizungulila jiko lonche la 
Havilah, pamwepo zahab ; 12 ndipo zahab 
ya pa jiko lija yabwino : pamwepo bedo- 
lah ndi mwala wa shoham. 13 Ndi jina 
la mchinje wa kawili Gihon : umwewo 
wakulizungulila jiko lonche la Kush. 
14 Ndi jina la mchinje wa katatu Hidde- 
kel: umwewo wakuyenda kwa kuvuma 
kwa Assur. Ndi mchinje wa kanai Eu- 
phrates. 15 Naajitengela Yahveh Mlungu 
muntu, naamsiilapo pa munda wa Eden 
kuulima ndi kuusunga. 16 Naamtaukila 
Yahveh Mlungu muntu, kuti, Va mtengo 
uli wonche wa pa munda kudya ujidya : 
17 nampo va mtengo wa kujiwa vabwino 
ndi voipa, usadya : chifuko pa siku ilo 
suudyeko kufa suufe. 

18 Naati Yahveh Mlungu, Yosali ya- 
bwino muntu akale pa yeka ; sindi- 
mchitile wakumtangatila kuanjana naye. 
19 Naachiumba Yahveh Mlungu kucho- 
kela pa ntaka, chikoko chili chonche cha 
pa dambo, ndi chakuuluka chili chonche 
cha Kumwamba ; naaja nazo kwa muntu 
kuona akadazitana chiani : ndipo lili 
lonche muntu adachitana chene umoyo 
chili chonche chakulama, limwelo linali 
jina lake. 20 Naatana muntu chilangwa 
chonche majina, ndi chakuuluka cha Ku- 
mwamba, ndi chikoko chili chonche cha pa 
dambo ; nampo kwa muntu wosakomanika 
wakumtangatila kuanjana naye. 21 Naa- 
mgwechela Yahveh Mlungu litulo lakule- 
mela pamwamba pa muntu, naagona litulo; 
naatenga imoji ya ntiti zake, naacheka- 
ncho nyama pa malo pake : 22 naama- 
nga Yahveh Mlungu ntiti iyo anaitenga 



GENESIS 



2. 23—4. 6 



pa muntu, kukala wamkazi, naaja naye 
kwa muntu. 23 Naati muntu, Uyu 
nyengo ii fupa la mafupa yanga, ndi 
nyama ya nyama yanga : uyu satanidwe 
Muntu Mkazi, chifuko anatengedwa pa 
Muntu uyu. 24 Mmwemo muntu samsie 
atate wake ndi amake, ndi sakanilile ndi 
mkazake : ndipo siwapate kukala nyama 
imoji. 25 Niwakala wonche wawili ma- 
liseehe, muntu ndi mkazake, ndi wosa- 
onana manyazi. 

8 Ndi njoka idali yochenjela kupunda 
chikoko chili chonche cha pa dambo 
icho Yahveh Mlungu anachichita. Naati 
kwa wamkazi Kodi Mlungu anati, Si- 
mngadye pa mtengo uli wonche wa 
munda ? 2 Naati wamkazi kwa njoka, 
Tikoza kudyelako vipacho va mitengo ya 
pa munda : 3 nampo vipacho va mte- 
ngo uwo uli pakati pa munda, adati 
Mlungu, Simngadye, simngapapase, mnga- 
fe. 4 Naati njoka kwa wamkazi, Kufa si- 
mngafe : 5 chifuko Mlungu ajiwa kuti 
siku ilo simdyeko, ndipo siyaehekulidwe 
maso yanu, ndipo simkale ngati achi- 
mlungu, kujiwa vabwino ndi voipa. 
6 Naaona wamkazi kuti mtengo udali 
wabwino kwa kudya, ndi kuti umwewo 
wakukonda pa maso, ndi wokumbika 
mtengo kujilingila, naajitengela vipacho 
vake, naadya ; naamninkao mwamunake 
pamoji naye, naadya. 7 Ndipo maso 
ya wonche wawili yadachekulidwa, niwa- 
jiwa kuti wali maliseche ; niwasoka ma- 
chamba ya mkuyu pamoji, niwajichitila 
chakunung'umala. 8 Niwaliva pokoso la 
Yahveh Mlungu naayendayenda pa mu- 
nda pa nyengo yake mpepo : naabisala 
muntu ndi mkazake pa nkope ya Yahveh 
Mlungu pakati pa mitengo ya pa munda. 
9 Naamtana Yahveh Mlungu muntu, 
naati kwa iye, Uli kuti ? 10 Naati, 
Ndidaliva pokoso lako pa munda, ndipo 
ndidaopa, chifuko ndili maliseche ; ndipo 
ndidabisala. 11 Naati, Yani adakuuza 
kuti uli maliseche? Kodi unadya va 
mtengo, uwo ndidakutaukila kuti usadya ? 
12 Naati muntu, Wamkazi uyo udandi- 
ninka kukala ndi ine, mmweyo adanini- 
nka va mtengo, ndipo ndidadya. 13 Na- 
ati Yahveh Mlungu kwa wamkazi, Chiani 
ichi udachichita? Naati wamkazi 
Njoka * adandinyenga, ndipo ndidadya 
14 Naati Yahveh Mlungu kwa njoka 
Chifuko udachita ichi, unalesweka kupu- 
nda chilangwa chili chonche, ndi kupunda 



chikoko chili chonche cha kudambo ; pa 
mimba yako suuyende, ndipo lifumbi 
suudye masiku yonche ya kulama kwako : 

15 ndipo sinditile mawongo pakati pa 
iwe ndi wamkazi, ndi pakati pa mbeu 
yako ndi mbeu yake : iye sakukotole 
mutu, ndi iwe suumkotole chidende. 

16 Kwa wamkazi adati, Kuchurukicha 
sindichurukiche kupweteka kwako ndi 
kuima mimba kwako ; pa vopweteka suu- 
pume wana ; ndi kukumbila kwako siku- 
kale kwa mwamunako, ndipo iye sakuli- 
nganichile. 17 Ndipo kwa muntu adati, 
Pakuti unava mau ya mkazako, ndi una- 
dya va mtengo, uwo ndidakutaukila, kuti, 
Usadya : ntaka yalesweka chifuko chako ; 
pa kupweteka suudyepo masiku yonche 
ya kulama kwako ; 18 mingancho ndi 
chiteji silikupukichile ; ndi suudye mmela 
wa munda ; 19 pa chitukuta cha pa 
mpuno zako suudye chakudya, mpaka 
sudabwelele pa ntaka ; pakuti udatenge- 
dwa mmwemo : pakuti lifumbi uli, ndipo 
ku lifumbi subwelelencho. 20 Naatana 
muntu jina la mkazake Hawa; pakuti 
adali amai wa ali yenche wakulama. 
21 Naawachitila Yahveh Mlungu muntu 
ndi mkazake vakuvinikila va vikwetu, 
naawavalika. 

22 Naati Yahveh Mlungu, Penya, muntu 
anapata kukala ngati mmoji wa ife, kujiwa 
vabwino ndi voipa ; ndipo chapano, anga- 
tambasule janja lake, ndi kujitengelancho 
va mtengo wa kulama, ndi kudya, ndi 
kulamila chikalile mmwemoje : 23 ndipo 
Yahveh Mlungu adampacha mwanja 
achoke pa munda wa Eden, kulima pa 
ntaka yapo adatengedwa. 24 Naamtopola 
muntu ; naaika A-Kerub kuvuma ku 
munda wa Eden, ndi lilime la moto la 
upanga wakujilozecha konche konche, 
kuisunga njila ya mtengo wa kulama. 



CHIKALAKALA CHOYEEA 



NDICHO 



MALANGANO YA KALE 



NDI 



MALANGANO YA CHAPANO 

LONDON 
BKITISH AND FOREIGN BIBLE SOCIETY 

1912